2 Mbiri 24:7 BL92

7 Pakuti ana a Ataliya mkazi woipa uja anathyola citseko ca nyumba ya Mulungu, natenga zopatulidwa zonse za nyumba ya Yehova kuzipereka kwa Baala.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 24

Onani 2 Mbiri 24:7 nkhani