2 Mbiri 25:11 BL92

11 Nalimbika mtima Amaziya, natsogolera anthu ace, namuka ku Cigwa ca Mcere, nakantha ana a Seiri zikwi khumi.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 25

Onani 2 Mbiri 25:11 nkhani