10 Pamenepo Amaziya anawapambutsa, ndiwo ankhondo anamdzera kucokera ku Efraimu, amuke kwao; potero adapsa mtima kwambiri pa Yuda, nabwera kwao ndi kutentha mtima.
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 25
Onani 2 Mbiri 25:10 nkhani