9 Ndipo Amaziya anati kwa munthu wa Mulungu, Koma nanga titani nao matalente zana limodzi ndinapatsa ankhondo a Israyeli? Nati munthu wa Mulungu, Yehova ali nazo zoposa izi kukupatsani.
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 25
Onani 2 Mbiri 25:9 nkhani