2 Mbiri 25:8 BL92

8 Koma ngati mumuka, citani, limbikani kunkhondo, Mulungu adzakugwetsani pamaso pa adani; pakuti Mulungu ali nayo mphamvu yakuthandiza ndi yakugwetsa.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 25

Onani 2 Mbiri 25:8 nkhani