7 Koma anamdzera munthu wa Mulungu, kuti, Mfumu, khamu la nkhondo la Israyeli lisapite nanu; pakuti Yehova sakhala ndi Israyeli, sakhala ndi ana onse a Efraimu.
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 25
Onani 2 Mbiri 25:7 nkhani