2 Mbiri 25:13 BL92

13 Koma amuna a nkhondo amene Amaziya anawabwereretsa, kuti asamuke naye kunkhondo, anagwera midzi ya Yuda kuyambira Samariya kufikira Betihoroni, nakantha a iwowa zikwi zitatu, nalanda zofunkha zambiri.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 25

Onani 2 Mbiri 25:13 nkhani