2 Mbiri 25:14 BL92

14 Ndipo kunali, atafika Amaziya atatha kuwapha Aedomu, ndi kubwera nayo milungu ya ana a Seiri, anaiika ikhale milungu yace, naigwadira, naifukizira,

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 25

Onani 2 Mbiri 25:14 nkhani