2 Mbiri 25:15 BL92

15 Pamenepo mkwiyo wa Mulungu unayakira Amaziya, ndipo anamtumira mneneri amene anati, Mwafuniranji milungu ya anthu imene siinalanditsa anthu ao m'dzanja lanu?

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 25

Onani 2 Mbiri 25:15 nkhani