26 Macitidwe ena tsono a Amaziya, oyamba ndi otsiriza, taonani, salembedwa kodi m'buku la mafumu a Yuda ndi Israyeli?
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 25
Onani 2 Mbiri 25:26 nkhani