27 Ndipo cipambukire Amaziya kusatsata Yehova, anamcitira ciwembu m'Yerusalemu, nathawira ku Lakisi iyeyu; koma anatuma omtsatira ku Lakisi, namupha komweko.
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 25
Onani 2 Mbiri 25:27 nkhani