2 Mbiri 28:1 BL92

1 Ahazi anali wa zaka makumi awiri polowa ufumu wace, nakhala mfumu m'Yerusalemu zaka khumi mphambu zisanu ndi cimodzi; koma sanacita zoongoka pamaso pa Yehova ngati Davide kholo lace,

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 28

Onani 2 Mbiri 28:1 nkhani