17 Ndipo anaimiritsa nsanamirazo pakhomo pa Kacisi; imodzi ku dzanja lamanja, ndi inzace ku dzanja lamanzere; nalicha dzina la iyi ya ku dzanja lamanja Yakini, ndi dzina la iyi ya ku dzanja lamanzere Boazi.
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 3
Onani 2 Mbiri 3:17 nkhani