2 Mbiri 4:1 BL92

1 Anapanganso guwa la nsembe lamkuwa, m'litali mwace mikono makumi awiri, ndi kupingasa kwace mikono makumi awiri, ndi msinkhu wace mikono khumi.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 4

Onani 2 Mbiri 4:1 nkhani