2 Mbiri 30:15 BL92

15 Pamenepo anaphera Paskha tsiku lakhumi ndi cinai la mwezi waciwiri, ndipo ansembe ndi Alevi anacita manyazi, nadzipatula, nabwera nazo nsembe zopsereza ku nyumba ya Yehova.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 30

Onani 2 Mbiri 30:15 nkhani