2 Mbiri 30:16 BL92

16 Naima m'malo mwao mwa kulongosoka kwao, monga mwa cilamulo ca Mose munthu wa Mulunguyo; ansembe anawaza mwazi, ataulandira ku dzanja la Alevi.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 30

Onani 2 Mbiri 30:16 nkhani