2 Mbiri 30:17 BL92

17 Pakuti munali ambiri mumsonkhano sanadzipatula; potero Alevi anayang'anira kupha za Paskha kwa ali yense wosakhala woyera, kuwapatulira Yehova.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 30

Onani 2 Mbiri 30:17 nkhani