2 Mbiri 32:22 BL92

22 Momwemo Yehova analanditsa Hezekiya ndi okhala m'Yerusalemu m'dzanja la Sanakeribu mfumu ya Asuri, ndi m'dzanja la onse ena, nawatsogolera monsemo.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 32

Onani 2 Mbiri 32:22 nkhani