26 Koma Hezekiya anadzicepetsa m'kudzikuza kwa mtima wace, iye ndi okhala m'Yerusalemu, momwemo mkwiyo wa Yehova sunawadzera masiku a Hezekiya.
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 32
Onani 2 Mbiri 32:26 nkhani