27 Ndipo cuma ndi ulemu zinacurukira Hezekiya, nadzimangira iye zosungiramo siliva, ndi golidi, ndi timiyala ta mtengo wace, ndi zonunkhira, ndi zikopa, ndi zipangizo zokoma ziri zonse;
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 32
Onani 2 Mbiri 32:27 nkhani