30 Hezekiya yemweyo anatseka kasupe wa kumtunda wa madzi a Gihoni, nawapambutsa atsikire ku madzulo kwa mudzi wa Davide. Ndipo Hezekiya analemerera nazo nchito zace zonse.
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 32
Onani 2 Mbiri 32:30 nkhani