2 Mbiri 32:31 BL92

31 Koma pokhala naye akazembe a akalonga a ku Babulo, amene anatumiza kwa iye kufunsira za codabwiza cija cidacitika m'dzikomo, Mulungu anamsiya, kumuyesa, kuti adziwe zonse za mumtima mwace.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 32

Onani 2 Mbiri 32:31 nkhani