13 Anampempha, ndipo anapembedzeka, namvera kupembedza kwace, nambwezera ku Yerusalemu m'ufumu wace. Pamenepo anadziwa Manase kuti Yehova ndiye Mulungu.
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 33
Onani 2 Mbiri 33:13 nkhani