15 Ndipo anacotsa milungu yacilendo, ndi fanoli m'nyumba ya Yehova, ndi maguwa onse a nsembe anawamanga m'phiri la nyumba ya Yehova ndi m'Yerusalemu, nawataya kunja kwa mudzi.
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 33
Onani 2 Mbiri 33:15 nkhani