20 Momwemo Manase anagona ndi makolo ace, namuika m'nyumba mwace mwace; ndi Amoni mwana wace anakhala mfumu m'malo mwace.
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 33
Onani 2 Mbiri 33:20 nkhani