2 Mbiri 35:14 BL92

14 Ndi pambuyo pace anadzikonzera okha ndi ansembe; popeza ansembe, ana a Aroni, analikupereka nsembe zopsereza ndi mafuta mpaka usiku; cifukwa cace Alevi anadzikonzera okha ndi ansembe ana a Aroni.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 35

Onani 2 Mbiri 35:14 nkhani