2 Mbiri 35:4 BL92

4 Ndipo mudzikonzere monga mwa nyumba za makolo anu, m'zigawo zanu, monga umo adalembera Davide mfumu ya Israyeli, ndi umo adalembera Solomo mwana wace.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 35

Onani 2 Mbiri 35:4 nkhani