2 Mbiri 35:5 BL92

5 Ndipo muimirire m'malo opatulika, monga mwa magawidwe a nyumba za makolo za abale anu ana a anthu, akhale nalo onse gawo la nyumba ya makolo ya Alevi.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 35

Onani 2 Mbiri 35:5 nkhani