6 Ndipo muphere Paskha, nimudzipatule ndi kukonzera abale anu, kucita monga mwa mau a Yehova ndi dzanja la Mose.
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 35
Onani 2 Mbiri 35:6 nkhani