2 Mbiri 35:7 BL92

7 Ndipo Yosiya anapatsa ana a anthu zoweta, ana a nkhosa ndi a mbuzi zikhale zonsezo za nsembe za Paskha kwa ali yense anali komweko; zinafikira zikwi makumi atatu, ndi ng'ombe zikwi zitatu, ndizo zotapa pa cuma ca mfumu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 35

Onani 2 Mbiri 35:7 nkhani