2 Mbiri 36:10 BL92

10 Ndipo pofikanso nyengo, mfumu Nebukadinezara anatumiza anthu abwere naye ku Babulo, pamodzi ndi zipangizo zokoma za nyumba ya Yehova; nalonga Zedekiya mbale wace mfumu ya Yuda ndi Yerusalemu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 36

Onani 2 Mbiri 36:10 nkhani