9 Yehoyakini anali wa zaka zisanu ndi zitatu polowa ufumu wace, nakhala mfumu m'Yerusalemu miyezi itatu, ndi masiku khumi; nacita coipa pamaso pa Yehova.
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 36
Onani 2 Mbiri 36:9 nkhani