19 Cinkana citero, labadirani pemphero la kapolo wanu, ndi pembedzero lace, Yehova Mulungu wanga, kumvera kupfuula ndi kupempha kwace, kumene kapolo wanu apempha pamaso panu;
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 6
Onani 2 Mbiri 6:19 nkhani