2 Mbiri 6:20 BL92

20 kuti maso anu atsegukire nyumba iyi usana ndi usiku, malo amene munanenerako kuti mudzaikako dzina lanu, kuti mumvere pemphero limene kapolo wanu adzapempha kuloza konkuno.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 6

Onani 2 Mbiri 6:20 nkhani