36 Akacimwira Inu (pakuti palibe munthu wosacimwa), nimukakwiya nao, ndi kuwapereka kwa adani, kuti awatenge andende kumka nao ku dziko lakutali, kapena lapafupi;
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 6
Onani 2 Mbiri 6:36 nkhani