37 koma akalingirira m'mtima mwao kudziko kumene anawatengera andende, nakatembenuka, nakapembedzera Inu m'dziko la undende wao, ndi kuti, Tacimwa, tacita mphulupulu, tacita coipa;
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 6
Onani 2 Mbiri 6:37 nkhani