2 Mbiri 6:38 BL92

38 akabwerera kwa Inu ndi mtima wao wonse, ndi moyo wao wonse, m'dziko la undende wao, kumene adawatengera andende; nakapemphera kuloza ku dziko lao limene munapatsa makolo ao, ndi mudzi mudausankha, ndi kunyumba ndamangira dzina lanuyi;

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 6

Onani 2 Mbiri 6:38 nkhani