39 pamenepo mumvere Inu m'Mwamba mokhala Inumo pemphero lao ndi pembedzero lao, ndi kulimbitsa mlandu wao; nimukhululukire anthu anu amene anakucimwirani.
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 6
Onani 2 Mbiri 6:39 nkhani