2 Mbiri 27:1 BL92

1 Yotamu anali wa zaka makumi awiri, mphambu zisanu polowa ufumu wace, nakhala mfumu m'Yerusalemu zaka khumi ndi zisanu ndi cimodzi; ndi dzina la mace ndiye Yerusa mwana wa Zadoki.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 27

Onani 2 Mbiri 27:1 nkhani