18 Macitidwe ena tsono a Manase, ndi pemphero lace kwa Mulungu wace, ndi mau a alauli akunena naye m'dzina la Yehova Mulungu wa Israyeli, taonani, zalembedwa m'niacitidwe a mafumu a Israyeli.
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 33
Onani 2 Mbiri 33:18 nkhani