2 Mbiri 8:10 BL92

10 Amenewa anali akuru a akapitao a mfumu Solomo, ndiwo mazana awiri mphambu makumi asanu akulamulira anthu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 8

Onani 2 Mbiri 8:10 nkhani