9 Koma mwa ana a Israyeli Solomo sanawayesa akapolo omgwirira nchito; koma iwowa anali anthu a nkhondo, akazembe ace akuru, ndi akuru a magareta ace, ndi apakavalo ace.
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 8
Onani 2 Mbiri 8:9 nkhani