Eksodo 1:17 BL92

17 Koma anamwino anaopa Mulungu, ndipo sanacita monga mfumu ya Aigupto inawauza, koma analeka ana amuna akhale ndi moyo.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 1

Onani Eksodo 1:17 nkhani