21 Ndipo Yehova anati kwa Mose, Tambasulira dzanja lako kuthambo, ndipo padzakhala mdima pa dziko la Aigupto, ndiwo mdima wokhudzika.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 10
Onani Eksodo 10:21 nkhani