24 Ndipo Farao anaitana Mose, nati, Mukani, tumikirani Yehova; nkhosa zanu ndi ng'ombe zanu zokha zitsale; mumuke nao ana anu ang'ononso.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 10
Onani Eksodo 10:24 nkhani