18 Mwezi woyamba, tsiku lace lakhumi ndi cinai madzulo ace, muzidya mkate wopanda cotupitsa, kufikira tsiku la makumi awiri mphambu limodzi la mwezi, madzulo ace.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 12
Onani Eksodo 12:18 nkhani