4 Banja likaperewera mwana wa nkhosa, munthu ndi mnzace ali pafupi pa nyumba yace atenge monga mwa kufikira kwa anthu ao; muziwerengera mwana wa nkhosa monga mwa kudya kwao.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 12
Onani Eksodo 12:4 nkhani