7 Ndipo azitengako mwazi, naupake pa mphuthu za mbali ndi ya pamwamba m'nyumba zimene adyeramo.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 12
Onani Eksodo 12:7 nkhani