16 Ndipo cizikhala ngati cizindikilo pa dzanja lako, ndi capamphumi pakati pa maso ako; pakuti Yehova anatiturutsa m'Aigupto ndi dzanja lamphamvu.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 13
Onani Eksodo 13:16 nkhani