Eksodo 13:18 BL92

18 Koma Mulungu anawazungulitsa anthuwo, ku njira ya kucipululu ya Nyanja Yofiira; ndipo ana a Israyeli anakwera kucokera m'dziko la Aigupto okonzeka.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 13

Onani Eksodo 13:18 nkhani